Mateyu 6:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo ndani wa inu ndi kudera nkhawa angathe kuonjezera pa msinkhu wake mkono umodzi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo ndani wa inu ndi kudera nkhawa angathe kuonjezera pa msinkhu wake mkono umodzi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Ndani mwa inu ndi maganizo ankhaŵa angathe kuwonjezera ngakhale tsiku limodzi pa moyo wake? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kodi ndani wa inu podandaula angathe kuwonjeza ora limodzi pa moyo wake? Onani mutuwo |