Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 6:18 - Buku Lopatulika

18 kuti usaonekere kwa anthu kuti ulikusala kudya, koma kwa Atate wako ali m'tseri: ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 kuti usaonekere kwa anthu kuti ulikusala kudya, koma kwa Atate wako ali m'tseri: ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 kuti anthu asadziŵe kuti ukusala zakudya. Koma Atate ako amene ali osaoneka ndiwo adziŵe. Ndipo Atate akowo amene amaona zobisika, adzakupatsa mphotho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 kuti usaonekere kwa anthu kuti ukusala kudya koma kwa Atate ako ali mseri; ndipo Atate ako amene amaona za mseri adzakupatsa mphotho.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 6:18
8 Mawu Ofanana  

kotero kuti mphatso zako zachifundo zikhale zam'tseri; ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.


Koma iwe popemphera, lowa m'chipinda chako, nutseke chitseko chako, nupemphere Atate wako ali m'tseri, ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.


amene adzabwezera munthu aliyense kolingana ndi ntchito zake;


pakuti si iye amene adzitama yekha, koma iye amene Ambuye amtama ali wovomerezeka.


Chifukwa chakenso tifunitsitsa, kapena kwathu kapena kwina, kukhala akumkondweretsa Iye.


kuti mayesedwe a chikhulupiriro chanu, ndiwo a mtengo wake woposa wa golide amene angotayika, ngakhale ayesedwa ndi moto, akapezedwe ochitira chiyamiko ndi ulemerero ndi ulemu pa vumbulutso la Yesu Khristu;


Tadzigonjani kwa zoikika zonse za anthu, chifukwa cha Ambuye; ngakhale kwa mfumu, monga mutu wa onse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa