Mateyu 6:14 - Buku Lopatulika14 Pakuti ngati mukhululukira anthu zolakwa zao adzakhululukira inunso Atate wanu wa Kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pakuti ngati mukhululukira anthu zolakwa zao adzakhululukira inunso Atate wanu wa Kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 “Ndithu ngati mukhululukira anthu machimo ao, Atate anu akumwamba adzakukhululukirani inunso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ngati inu mukhululukira anthu pamene akuchimwirani, Atate anu akumwamba adzakukhululukirani. Onani mutuwo |