Mateyu 6:15 - Buku Lopatulika15 Koma ngati simukhululukira anthu zolakwa zao, Atate wanunso sadzakhululukira zolakwa zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma ngati simukhululukira anthu zolakwa zao, Atate wanunso sadzakhululukira zolakwa zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Koma ngati simukhululukira anthu machimo ao, Atate anunso sadzakukhululukirani machimo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Koma ngati inu simukhululukira anthu zolakwa zawo, Atate anunso sadzakukhululukirani machimo anu. Onani mutuwo |