Mateyu 6:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso takhululukira amangawa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso takhululukira amangawa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mutikhululukire ife machimo athu, monga ifenso takhululukira otilakwira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso tawakhululukira amangawa athu. Onani mutuwo |