Mateyu 6:11 - Buku Lopatulika11 Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Mutipatse ife lero chakudya chathu chalero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mutipatse ife lero chakudya chathu chamasikuwonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mutipatse chakudya chathu chalero. Onani mutuwo |