Mateyu 5:6 - Buku Lopatulika6 Odala ali akumva njala ndi ludzu la chilungamo; chifukwa adzakhuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Odala ali akumva njala ndi ludzu la chilungamo; chifukwa adzakhuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ngodala anthu amene akumva njala ndi ludzu lofuna chilungamo, pakuti Mulungu adzakwaniritsa zofuna zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Odala ndi amene akumva njala ndi ludzu la chilungamo, chifukwa adzakhutitsidwa. Onani mutuwo |