Mateyu 5:7 - Buku Lopatulika7 Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ngodala anthu ochitira anzao chifundo, pakuti iwonso Mulungu adzaŵachitira chifundo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Odala ndi amene ali ndi chifundo, chifukwa adzawachitira chifundo. Onani mutuwo |