Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 5:47 - Buku Lopatulika

47 Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

47 Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

47 Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okha, mwachitapo chiyani pamenepo choposa ena? Kodi suja ngakhale akunja amachita chimodzimodzi?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

47 Ndipo ngati inu mupatsa moni abale anu okhaokha mukuchita chiyani choposa ena? Kodi ngakhale akunja sachita chimodzimodzi?

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 5:47
9 Mawu Ofanana  

Ndipo polowa m'nyumba muwalonjere.


Pakuti ndinena ndi inu, ngati chilungamo chanu sichichuluka choposa cha alembi ndi Afarisi, simudzalowa konse mu Ufumu wa Kumwamba.


Chifukwa kuti ngati muwakonda akukondana ndi inu mphotho yanji muli nayo? Kodi angakhale amisonkho sachita chomwecho?


Chifukwa chake inu mukhale angwiro, monga Atate wanu wa Kumwamba ali wangwiro.


Ndipo ngati muwakonda iwo akukondana ndinu, mudzalandira chiyamiko chotani? Pakuti ochimwa omwe akonda iwo akukondana nao.


Akupatsani moni Luka sing'anga wokondedwa, ndi Dema.


Perekani moni kwa abalewo a mu Laodikea, ndi Nimfa, ndi Mpingowo wa m'nyumba yao.


Pakuti mbiri yokoma yanji, mukapirira pochimwa ndi kubwanyulidwapo? Komatu, ngati pochita zabwino, ndi kumvako ndiko chisomo pa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa