Mateyu 5:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo amene akakukakamiza kumperekeza njira imodzi, upite naye ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo amene akakukakamiza kumperekeza njira imodzi, upite naye ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Munthu akakukakamiza kuyenda naye mtunda umodzi, uyende naye mitunda iŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Ngati wina akukakamiza kuti uyende naye mtunda umodzi, iwe uyende naye mitunda iwiri. Onani mutuwo |