Mateyu 5:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo kwa iye wofuna kupita nawe kumlandu ndi kutenga malaya ako, umlolezenso chofunda chako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo kwa iye wofuna kupita nawe kumlandu ndi kutenga malaya ako, umlolezenso chofunda chako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Munthu akakuzenga mlandu nafuna kukulanda mkanjo wako, umlole atengenso ndi mwinjiro wako womwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Ndipo ngati wina afuna kukuzenga mlandu kuti akulande malaya ako, umupatsenso mkanjo wako. Onani mutuwo |