Mateyu 5:39 - Buku Lopatulika39 koma ndinena kwa inu, Musakanize munthu woipa; koma amene adzakupanda iwe pa tsaya lako lamanja, umtembenuzire linanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 koma ndinena kwa inu, Musakanize munthu woipa; koma amene adzakupanda iwe pa tsaya lako lamanja, umtembenuzire linanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Chabwino, koma Ine ndikukuuzani kuti munthu woipa osalimbana naye. Ngati munthu akumenya pa tsaya la ku dzanja lamanja, upereke linalonso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Koma ndikuwuzani kuti musamukanize munthu woyipa, akakumenya patsaya mupatseni tsaya linalo. Onani mutuwo |