Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 5:38 - Buku Lopatulika

38 Munamva kuti kunanenedwa, Diso kulipa diso, ndi dzino kulipa dzino:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

38 Munamva kuti kunanenedwa, Diso kulipa diso, ndi dzino kulipa dzino:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

38 “Mudamva kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Diso kulipa diso, dzino kulipa dzino.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

38 “Munamva kuti, ‘Diso kulipira diso ndi dzino kulipira dzino.’

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 5:38
6 Mawu Ofanana  

Munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usaphe; koma yense wakupha adzakhala wopalamula mlandu:


Munamva kuti kunanenedwa, Usachite chigololo;


mumchitire monga iye anayesa kumchitira mbale wake; motero muchotse choipacho pakati panu.


Ndipo diso lanu lisachite chifundo, moyo kulipa moyo, diso kulipa diso, dzino kulipa dzino, dzanja kulipa dzanja, phazi kulipa phazi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa