Mateyu 5:21 - Buku Lopatulika21 Munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usaphe; koma yense wakupha adzakhala wopalamula mlandu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Munamva kuti kunanenedwa kwa iwo akale, Usaphe; koma yense wakupha adzakhala wopalamula mlandu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 “Mudamva kuti anthu akale aja adaaŵalamula kuti, ‘Usaphe. Aliyense wopha mnzake adzayenera kuzengedwa ku bwalo lamilandu,’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 “Munamva kuti kunanenedwa kwa anthu kale kuti, ‘Usaphe ndipo kuti aliyense amene apha munthu adzaweruzidwa.’ Onani mutuwo |