Mateyu 5:17 - Buku Lopatulika17 Musaganize kuti ndinadza Ine kudzapasula chilamulo kapena aneneri: sindinadze kupasula, koma kukwaniritsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Musaganize kuti ndinadza Ine kudzapasula chilamulo kapena aneneri: sindinadza kupasula, koma kukwaniritsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 “Musamaganiza kuti ndidadzathetsa Malamulo a Mose ndiponso zophunzitsa za aneneri. Inetu sindidadzere kudzaŵathetsa, koma kudzaŵafikitsa pachimake penipeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Musaganize kuti ndinadza kudzathetsa malamulo kapena zonena za aneneri; sindinabwere kudzathetsa koma kukwaniritsa. Onani mutuwo |