Mateyu 4:8 - Buku Lopatulika8 Pomwepo mdierekezi anamuka naye kuphiri lalitali, namuonetsa maufumu onse a dziko lapansi, ndi ulemerero wao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pomwepo mdierekezi anamuka naye kuphiri lalitali, namuonetsa maufumu onse a dziko lapansi, ndi ulemerero wao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Potsiriza Satana adatenga Yesu kupita naye pa phiri lalitali kwambiri, ndipo adamuwonetsa maufumu onse a pansi pano ndi ulemerero wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kenaka mdierekezi anamutengera Yesu ku phiri lalitali kwambiri namuonetsa maufumu onse a dziko lapansi ndi ulemerero wawo. Onani mutuwo |