Mateyu 4:16 - Buku Lopatulika16 anthu akukhala mumdima adaona kuwala kwakukulu, ndi kwa iwo okhala m'malo a mthunzi wa imfa, kuwala kunatulukira iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 anthu akukhala mumdima adaona kuwala kwakukulu, ndi kwa iwo okhala m'malo a mthunzi wa imfa, kuwala kunatulukira iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Anthu okhala mu mdima aona kuŵala kwakukulu. Anthu okhala m'dziko la mdima wabii wa imfa, kuŵala kwaŵaonekera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 anthu okhala mu mdima awona kuwala kwakukulu; ndi kwa iwo okhala mʼdziko la mthunzi wa imfa kuwunika kwawafikira.” Onani mutuwo |