Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 4:15 - Buku Lopatulika

15 Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, njira ya kunyanja, kutsidya lija la Yordani, Galileya wa anthu akunja,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, njira ya kunyanja, kutsidya lija la Yordani, Galileya la anthu akunja,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 “Iwe dziko la Zebuloni ndi iwe dziko la Nafutali, ku njira yakunyanja, patsidya pa Yordani, iwe Galileya, dziko la anthu akunja!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 “Dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, njira ya ku nyanja, kutsidya lija la Yorodani, Galileya wa anthu a mitundu ina,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 4:15
9 Mawu Ofanana  

popeza Hiramu mfumu ya Tiro adamthandiza Solomoni ndi mitengo yamkungudza ndi yamlombwa ndi golide yemwe, monga momwe iye anafuniramo, chifukwa chake mfumu Solomoni anampatsa Hiramu mizinda makumi awiri m'dziko la Galileya.


Masiku a Peka mfumu ya Israele anadza Tigilati-Pilesere mfumu ya Asiriya, nalanda Iyoni, ndi Abele-Beti-Maaka, ndi Yanowa, ndi Kedesi, ndi Hazori, ndi Giliyadi, ndi Galileya, dziko lonse la Nafutali; nawatenga andende kunka nao ku Asiriya.


Koma kumene kunali nsautso sikudzakhala kuziya. Poyamba paja Mulungu ananyozetsa dziko la Zebuloni, ndi dziko la Nafutali, koma potsiriza pake Iye analichitira ulemu, pa khwalala la kunyanja, patsidya pa Yordani, Galileya wa amitundu.


ndipo anachoka ku Nazarete nadza nakhalitsa Iye mu Kapernao wa pambali pa nyanja, m'malire a Zebuloni ndi Nafutali:


kuti chikachitidwe chonenedwa ndi Yesaya mneneri, kuti,


Ndipo inamtsata mipingomipingo ya anthu ochokera ku Galileya, ndi ku Dekapoli ndi ku Yerusalemu, ndi ku Yudeya, ndi ku tsidya lija la Yordani.


Ndipo anayamba kwa Mose, ndi kwa aneneri onse nawatanthauzira iwo m'malembo onse zinthu za Iye yekha.


Ndipo anapatula Kedesi mu Galileya ku mapiri a Nafutali, ndi Sekemu ku mapiri a Efuremu, ndi mudzi wa Ariba ndiwo Hebroni ku mapiri a Yuda.


Ndipo motapira pa fuko la Nafutali, Kedesi mu Galileya ndi mabusa ake, ndiwo mzinda wopulumukirako wakupha mnzakeyo, ndi Hamotidori ndi mabusa ake, ndi Karitani ndi mabusa ake, mizinda itatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa