Mateyu 3:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo masiku aja anadza Yohane Mbatizi, nalalikira m'chipululu cha Yudeya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo masiku aja anadza Yohane Mbatizi, nalalikira m'chipululu cha Yudeya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pa masiku amenewo kudaabwera Yohane Mbatizi nayamba kulalika m'chipululu cha ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mʼmasiku amenewo, Yohane Mʼbatizi anadza nalalikira mʼchipululu cha Yudeya Onani mutuwo |