Mateyu 2:23 - Buku Lopatulika23 nadza nakhazikika m'mzinda dzina lake Nazarete kuti chikachitidwe chonenedwa ndi aneneri kuti, Adzatchedwa Mnazarayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 nadza nakhazikika m'mudzi dzina lake Nazarete kuti chikachitidwe chonenedwa ndi aneneri kuti, Adzatchedwa Mnazarayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Kumeneko adakakhala ku mudzi wina dzina lake Nazarete, kuti zipherezere zimene aneneri adaanena kuti, “Adzatchedwa Mnazarete.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 ndipo anakakhazikika mu mzinda wa Nazareti. Pamenepo zinakwaniritsidwa zonenedwa ndi aneneri kuti, “Adzatchedwa Mnazareti.” Onani mutuwo |