Mateyu 28:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo iwo anachoka msanga kumanda, ndi mantha ndi kukondwera kwakukulu, nathamanga kukauza ophunzira ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo iwo anachoka msanga kumanda, ndi mantha ndi kukondwera kwakukulu, nathamanga kukauza ophunzira ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Apo azimaiwo adachoka kumandako msanga, ali ndi mantha komanso ndi chimwemwe chachikulu, nathamanga kukauza ophunzira ake aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamenepo amayiwo anachoka mofulumira ku mandako ali ndi mantha komabe atadzaza ndi chimwemwe, ndipo anathamanga kukawuza ophunzira ake. Onani mutuwo |