Mateyu 28:13 - Buku Lopatulika13 nati, Kazinenani, kuti ophunzira ake anadza usiku, namuba Uja m'mene ife tinali m'tulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 nati, Kazinenani, kuti ophunzira ake anadza usiku, namuba Uja m'mene ife tinali m'tulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 naŵauza kuti, “Muziti, ‘Ophunzira ake anabwera usiku nkuba mtembo wake ife tili m'tulo.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 nawawuza kuti, “Muzinena kuti, ‘Ophunzira ake anabwera usiku ndipo amuba ife tili mtulo.’ Onani mutuwo |