Mateyu 28:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo pamene anasonkhana pamodzi ndi akulu, anakhala upo, napatsa asilikaliwo ndalama zambiri, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo pamene anasonkhana pamodzi ndi akulu, anakhala upo, napatsa asilikaliwo ndalama zambiri, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono akulu a ansembe aja ndi akulu a Ayuda adasonkhana napangana nzeru. Adapatsa alonda aja ndalama zambiri, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Akulu a ansembe atakumana ndi akuluakulu anapangana zochita. Anapatsa alonda aja ndalama zambiri, Onani mutuwo |