Mateyu 28:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo pamene iwo analikupita, onani, ena a alonda anafika kumzinda, nauza ansembe aakulu zonse zimene zinachitidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo pamene iwo analikupita, onani, ena a alonda anafika kumzinda, nauza ansembe aakulu zonse zimene zinachitidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pamene akazi aja ankapita, ena mwa alonda aja adakafika ku mzinda, nakasimbira akulu a ansembe zonse zimene zidaachitika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Amayi aja akupita, ena mwa alonda aja anapita ku mzinda nafotokozera akulu a ansembe zonse zimene zinachitika. Onani mutuwo |