Mateyu 28:10 - Buku Lopatulika10 Pomwepo Yesu ananena kwa iwo, Musaope; pitani, kauzeni abale anga kuti amuke ku Galileya, ndipo adzandiona Ine kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pomwepo Yesu ananena kwa iwo, Musaope; pitani, kauzeni abale anga kuti amuke ku Galileya, ndipo adzandiona Ine kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Apo Yesu adaŵauza kuti, “Musaope. Pitani, kauzeni abale anga kuti apite ku Galileya. Akandiwonera kumeneko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo Yesu anawawuza kuti, “Musachite mantha, pitani kawuzeni abale anga kuti apite ku Galileya ndipo kumeneko akandiona Ine.” Onani mutuwo |