Mateyu 28:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo ngati ichi chidzamveka kwa kazembe, ife tidzamgwetsa mtima, ndipo tidzakukhalitsani opanda nkhawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo ngati ichi chidzamveka kwa kazembe, ife tidzamgwetsa mtima, ndipo tidzakukhalitsani opanda nkhawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho bwanamkubwa akamva zimenezi, ife tidzamkhazika mtima pansi, ndipo sipadzakhala kanthu kokuvutani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Ngati nkhani iyi imupeze bwanamkubwa, ife tidzamukhazika mtima pansi ndipo simudzakhala mʼmavuto.” Onani mutuwo |