Mateyu 27:8 - Buku Lopatulika8 Chifukwa chake munda umenewu anautcha, Munda-wa-mwazi, kufikira lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chifukwa chake munda umenewu anautcha, Munda-wa-mwazi, kufikira lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Nchifukwa chake mpaka lero mundawo umatchedwa “Munda wa Magazi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndi chifukwa chake umatchedwa munda wamagazi mpaka lero lino. Onani mutuwo |