Mateyu 27:7 - Buku Lopatulika7 Koma anapangana, nazigula munda wa woumba mbiya, ukhale manda a alendo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma anapangana, nazigula munda wa woumba mbiya, ukhale manda a alendo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Choncho adapangana kuti ndalamazo agulire munda wa mmisiri wa mbiya, kuti ukhale manda a alendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Choncho anagwirizana kuti ndalamazo azigwiritse ntchito pogulira munda wa wowumba mbiya kuti ukhale manda alendo. Onani mutuwo |