Mateyu 27:62 - Buku Lopatulika62 Ndipo m'mawa mwake, ndilo tsiku lotsatana ndi tsiku lokonzera, ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhana kwa Pilato, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201462 Ndipo m'mawa mwake, ndilo dzuwa lotsatana ndi tsiku lokonzera, ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanira kwa Pilato, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa62 M'maŵa mwake, litapita tsiku lokonzekera Sabata, akulu a ansembe pamodzi ndi Afarisi adasonkhana napita kwa Pilato. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero62 Litapita tsiku lokonzekera Sabata, mmawa mwake, akulu a ansembe ndi Afarisi anapita kwa Pilato. Onani mutuwo |