Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 27:61 - Buku Lopatulika

61 Ndipo Maria wa Magadala anali pamenepo, ndi Maria winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

61 Ndipo Maria wa Magadala anali pamenepo, ndi Maria winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

61 Maria wa ku Magadala ndi Maria wina uja anali pomwepo atakhala pansi kuyang'anana ndi mandawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

61 Mariya wa Magadala ndi Mariya wina anakhala pansi moyangʼanizana ndi mandawo.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 27:61
2 Mawu Ofanana  

mwa iwo amene munali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo, ndi wa Yosefe, ndi amake wa ana a Zebedeo.


Ndipo popita tsiku la Sabata, mbandakucha, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Maria wa Magadala, ndi Maria winayo, kudzaona manda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa