Mateyu 27:60 - Buku Lopatulika60 nauika m'manda ake atsopano, osemedwa m'mwala, nakunkhunizira mwala waukulu pakhomo pa manda, nachokapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201460 nauika m'manda ake atsopano, osemedwa m'mwala, nakunkhunizira mwala waukulu pakhomo pa manda, nachokapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa60 Adakauika m'manda ake atsopano ochita chosema m'thanthwe. Tsono adagubuduzira chimwala pa khomo kuti atseke pamandapo, nachoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero60 Ndipo anawuyika mʼmanda ake atsopano amene anasema mu thanthwe, natsekapo ndi mwala waukulu pa khomo la mandawo nachokapo. Onani mutuwo |