Mateyu 27:59 - Buku Lopatulika59 Ndipo Yosefe anatenga mtembo, naukulunga m'nsalu yabafuta yoyeretsa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201459 Ndipo Yosefe anatenga mtembo, naukulunga m'nsalu yabafuta yoyeretsa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa59 Tsono Yosefe adautenga, naukulunga m'nsalu yoyera yabafuta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero59 Yosefe anatenga mtembowo, nawukulunga nsalu yabafuta. Onani mutuwo |