Mateyu 27:57 - Buku Lopatulika57 Ndipo pamene panali madzulo, anadza munthu wachuma wa ku Arimatea, dzina lake Yosefe, amene analinso wophunzira wa Yesu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Ndipo pamene panali madzulo, anadza munthu wachuma wa ku Arimatea, dzina lake Yosefe, amene analinso wophunzira wa Yesu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Chisisira chitagwa, kudafika munthu wina wolemera, wochokera ku Arimatea, dzina lake Yosefe. Nayenso anali wophunzira wa Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Pamene kumada, kunabwera munthu wolemera wa ku Arimateyu dzina lake Yosefe amene anali wophunzira wa Yesu. Onani mutuwo |