Mateyu 27:58 - Buku Lopatulika58 yemweyo anapita kwa Pilato, napempha mtembo wa Yesu. Pomwepo Pilato analamula kuti uperekedwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201458 yemweyo anapita kwa Pilato, napempha mtembo wa Yesu. Pomwepo Pilato analamula kuti uperekedwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa58 Iyeyu adakapempha mtembo wa Yesu kwa Pilato. Pilato adalamula kuti ampatse mtembowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero58 Anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu, ndipo Pilato analamula kuti uperekedwe kwa iye. Onani mutuwo |