Mateyu 27:49 - Buku Lopatulika49 Koma ena anati, Taleka, tione ngati Eliya adzafika kudzampulumutsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Koma ena anati, Taleka, tione ngati Eliya adzafika kudzampulumutsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Koma ena adati, “Taima, tiwone ngati Eliya abweredi kudzampulumutsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Koma ena onse anati, “Mulekeni tiyeni tione ngati Eliyayo abwere kudzamupulutsa.” Onani mutuwo |