Mateyu 27:48 - Buku Lopatulika48 Ndipo pomwepa mmodzi wa iwo anathamanga, natenga chinkhupule, nachidzaza ndi vinyo wosasa, nachiika pabango, namwetsa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Ndipo pomwepa mmodzi wa iwo anathamanga, natenga chinkhupule, nachidzaza ndi vinyo wosasa, nachiika pabango, namwetsa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Motero wina adathamanga nakatenga chinkhupule. Adachiviika m'vinyo wosasa, nkuchitsomeka ku bango nampatsira, kuti amwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Mmodzi wa iwo anathamanga natenga chinkhupule. Anachidzaza ndi vinyo wosasa, nachizika ku mtengo namupatsa Yesu kuti amwe. Onani mutuwo |