Mateyu 27:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo ena a iwo akuimirira komweko, pamene anamva, ananena, Uyo aitana Eliya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo ena a iwo akuimirira komweko, pamene anamva, ananena, Uyo aitana Eliya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Atamva mauwo, ena amene adaaimirira pamenepo adati, “Munthuyu akuitana Eliya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Ena a oyimirira pamalopo atamva izi anati, “Akuyitana Eliya.” Onani mutuwo |