Mateyu 27:34 - Buku Lopatulika34 anamwetsa Iye vinyo wosakaniza ndi ndulu; ndipo Iye, m'mene analawa, sanafune kumwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 anamwetsa Iye vinyo wosanganiza ndi ndulu; ndipo Iye, m'mene analawa, sanafune kumwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Kumeneko adapatsa Yesu vinyo wosanganiza ndi ndulu kuti amwe. Koma atalaŵa, adakana kumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pamenepo anamupatsa vinyo wosakaniza ndi ndulu kuti amwe; koma atalawa anakana kumwa. Onani mutuwo |