Mateyu 27:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo pamene anadza kumalo dzina lake Gologota, ndiko kunena kuti, Malo a Bade, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo pamene anadza kumalo dzina lake Gologota, ndiko kunena kuti, Malo a Bade, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Ndipo adafika ku malo otchedwa Gologota, (ndiye kuti “Malo a Chibade cha Mutu.”) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Anafika ku malo wotchedwa Gologota amene atanthauza kuti malo a bade la mutu. Onani mutuwo |