Mateyu 27:26 - Buku Lopatulika26 Pomwepo iye anamasulira iwo Barabasi, koma anakwapula Yesu, nampereka Iye kuti akampachike pamtanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pomwepo iye anamasulira iwo Barabasi, koma anakwapula Yesu, nampereka Iye kuti akampachike pamtanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Apo Pilato adaŵamasulira Barabasi, nalamula kuti Yesu akwapulidwe. Pambuyo pake adampereka kuti akampachike pa mtanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pamenepo anawamasulira Baraba koma analamula kuti Yesu akakwapulidwe, ndipo anamupereka kuti akapachikidwe. Onani mutuwo |