Mateyu 27:20 - Buku Lopatulika20 Koma ansembe aakulu ndi akulu anapangira anthu kuti apemphe Barabasi, koma kuti aononge Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma ansembe aakulu ndi akulu anapangira anthu kuti apemphe Barabasi, koma kuti aononge Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Akulu a ansembe ndi akulu a Ayuda adayamba kukakamiza anthu kupempha Pilato kuti amasule Barabasi, ndipo kuti Yesu aphedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma akulu a ansembe ndi akuluakulu ananyengerera gulu la anthu kuti apemphe Baraba ndi kuti Yesu aphedwe. Onani mutuwo |