Mateyu 27:21 - Buku Lopatulika21 Koma kazembe anati kwa iwo, Mufuna kuti ndikumasulireni uti wa awa awiri? Ndipo iwo anati, Barabasi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma kazembe anati kwa iwo, Mufuna kuti ndikumasulireni uti wa awa awiri? Ndipo iwo anati, Barabasi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono bwanamkubwa uja adaŵafunsa kuti, “Mukufuna kuti ndikumasulireni uti mwa aŵiriŵa?” Anthu aja adati, “Barabasi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Bwanamkubwayo anafunsa kuti, “Ndi ndani mwa awiriwa amene mufuna ine ndikumasulireni?” Iwo anayankha kuti, “Baraba.” Onani mutuwo |