Mateyu 27:13 - Buku Lopatulika13 Pomwepo Pilato ananena kwa Iye, Sukumva kodi zinthu zambiri zotere akunenera Iwe? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pomwepo Pilato ananena kwa Iye, Sukumva kodi zinthu zambiri zotere akunenera Iwe? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Apo Pilato adamufunsa kuti, “Kodi sukumva zonse akukunenezazi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kenaka Pilato anamufunsa Iye kuti, “Kodi sukumva zinthu zimene akukunenerazi?” Onani mutuwo |