Mateyu 26:8 - Buku Lopatulika8 Koma m'mene ophunzira anaona, anada mtima, nanena, Chifukwa ninji kuononga kumeneku? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma m'mene ophunzira anaona, anada mtima, nanena, Chifukwa ninji kuononga kumeneku? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma pamene ophunzira ake adaona zimenezi, adaipidwa nazo nkumauzana kuti, “Chifukwa chiyani kusakaza zinthu chotere? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ophunzira ataona izi anayipidwa nafunsa kuti, “Chifukwa chiyani akuwononga chotere? Onani mutuwo |