Mateyu 26:72 - Buku Lopatulika72 Ndipo anakananso ndi chilumbiro, kuti, Sindidziwa munthuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201472 Ndipo anakananso ndi chilumbiro, kuti, Sindidziwa munthuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa72 Petro adakananso molumbira kuti, “Ndithudi sindikumdziŵa munthu ameneyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero72 Iye anakananso molumbira kuti, “Sindimudziwa munthuyu!” Onani mutuwo |