Mateyu 26:68 - Buku Lopatulika68 nati, Utilote ife, Khristu Iwe; wakumenya Iwe ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201468 nati, Utilote ife, Khristu Iwe; wakumenya Iwe ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa68 nkumanena kuti, “Iwe Mpulumutsi wolonjezedwa uja, nanga sindiwe mneneri? Lota, wakumenya ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero68 Ndipo anati, “Tanenera kwa ife, Khristu. Wakumenya ndani?” Onani mutuwo |