Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo pamene Yesu anali mu Betaniya, m'nyumba ya Simoni wakhate,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo pamene Yesu anali m'Betaniya, m'nyumba ya Simoni wakhate,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Tsiku lina Yesu anali ku Betaniya, m'nyumba ya Simoni wotchedwa Wakhate.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Yesu ali ku Betaniya mʼnyumba Simoni Wakhate,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:6
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Iye anawasiya, natuluka m'mzinda, napita ku Betaniya, nagona kumeneko.


Ndipo m'mawa mwake, atatuluka ku Betaniya, Iye anamva njala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa