Mateyu 26:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo pomwepo anadza kwa Yesu, nati, Tikuoneni, Rabi; nampsompsonetsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo pomwepo anadza kwa Yesu, nati, Tikuoneni, Rabi; nampsompsonetsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Tsono Yudasi adadzangofikira pa Yesu, nkunena kuti, “Moni Aphunzitsi!” Atatero adamumpsompsona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Pamenepo Yudasi anapita kwa Yesu nati, “Moni, Aphunzitsi!” Ndipo anapsompsona Iye. Onani mutuwo |