Mateyu 26:48 - Buku Lopatulika48 Koma wompereka Iye anawapatsa chizindikiro, nanena, Iye amene ndidzampsompsona ndiyeyo, mumgwire Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Koma wompereka Iye anawapatsa chizindikiro, nanena, Iye amene ndidzampsompsona ndiyeyo, mumgwire Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Wodzampereka uja anali ataŵauza chizindikiro kuti, “Yemwe ndikamumpsompsoneyo, ndi ameneyo, mukamugwire.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Womuperekayo anawawuziratu chizindikiro anthuwo kuti, “Amene ndidzapsompsona ndi iyeyo; mugwireni.” Onani mutuwo |