Mateyu 26:50 - Buku Lopatulika50 Ndipo Yesu anati kwa iye, Mnzanga, wafikiranji iwe? Pomwepo iwo anadza, namthira Yesu manja, namgwira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Ndipo Yesu anati kwa iye, Mnzanga, wafikiranji iwe? Pomwepo iwo anadza, namthira Yesu manja, namgwira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Yesu adamuuza kuti, “Bwenzi langa, chita zimene wadzera.” Apo anthu aja adabwera namugwira Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Yesu anayankha kuti, “Bwenzi langa, chita chimene wabwerera.” Pamenepo anthuwo anabwera patsogolo namugwira Yesu ndi kumumanga. Onani mutuwo |